Bungwe la Roads Fund Administration (RFA) lawopseza kuti oyendetsa galimoto omwe agwidwe akudutsa mokakamiza pa ma “tollgate” osalipira ndalama, alipira chindapusa cha ndalama yokwana 1 miliyoni kwacha. Izi ndi malingana ndi chikalata chomwe bungwe la RFA latulutsa Lachisanu chomwe chikuchenjeza onse oyendetsa galimoto za mtundu uli onse kuti asayesere dara kudutsa pa ma “tollgate” a […]
The post Mulipira K1 miliyoni mukathawa kulipira pa “tollgate” -yaopseza RFA appeared first on Malawi 24.