Chipatala cha Balaka chayamikira Ngalande popeleka galimoto

Pali chiyembekezo chachikulu kuti ntchito za umoyo m’boma la Balaka zipita patsogolo kutsatira thandizo la galimoto za ambulansi ziwiri zomwe phungu wa dera la kumpoto m’boma la Balaka, Tony Ngalande, wapeleka pa chipatala chachikulu cha bomali. Malingana ndi mneneri wa chipatalachi, Mercy Nyirenda, thandizoli lafika mu nthawi yomwe ngozi zosiyanasiyana zimachulukira. “Monga mukudziwa, tili mu […]

The post Chipatala cha Balaka chayamikira Ngalande popeleka galimoto appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください