Malawi24 yapeza kuti nkhani yomwe ikuyenda m’masamba a mchezo yoti anthu amagulitsa nyama ya galu ku Dowa siyinachitike ku Malawi. Pa masamba a mchezo a pa Fesibuku kuyambila dzulo madzulo pabuka nkhani yokuti anthu atatu amangidwa ku Dowa chifukwa anawapeza akugulitsa nyama ya galu yophikaphika pa chiwaya. Ena atengera nkhani yomweyi ku X komwe akuti […]
The post Mabodza: Nkhani ya nyama ya galu siyinachitike ku Malawi appeared first on Malawi 24.