Apolisi m’boma la Mchinji ati matumba a simenti okwana 186 ndi omwe apezeka pakadali pano pa matumba okwana 600 kutsatira pomwe thilaki yomwe idanyamula matumbawa idayaka moto kwa Kholoni mbomali. Thilakiyi yomwe ndi ya kampani ya Fermak idanyamula matumba a kampani ya AgriCom yomwe nambala yake ndi NS 1751 komanso telera yake ndi NS 5282 […]
The post Apolisi atolera matumba a simenti okwana 186 ku Mchinji appeared first on Malawi 24.