Mutale Mwanza yemwe ndi wachikondi wa oyimba odziwika bwino m’dziko lino, Tay Grin, wapulumuka pa ngozi yomwe inachitika dzulo pa 20 December ku Zambia. Nkhani yonse ikuti munthawi yomwe ngoziyi imachitika, a Mutale Mwanza amayendera pa galimoto ya mtundu wa Toyota Fortuner yomwe inawombana ndi galimoto ya mtundu wa Toyota Hilux yomwe inali pa tsogolo […]
The post Mutale Mwanza wapulumuka pa ngozi ya pamsewu appeared first on Malawi 24.