Apolisi m’boma la Machinga akhazikitsa makomiti owona zachitetezo cha m’madera a kumidzi m’bomalo pofuna kuchepetsa umbava ndi umbanda munyengo ino yachikondwelero cha khirisimasi komanso chaka chatsopano. Poyankhula pamwambo omwe amakhadzikitsa komiti yowoona zachitetedzo chamadera akumudzi mdera la T/A Mtumbwinda mkulu woona zachitetedzo chamadera akumudzi ku Police ya Machinga Masautso Katemera walangiza komiti yatsopanoyo kuti idzigwira […]
The post Apolisi ku Machinga akhazikitsa makomiti owona zachitetezo cha m’madera appeared first on Malawi 24.