Kuyelekeza ndi mchaka cha 2017 pomwe oyimba otchuka Dan Lufani anatchuka ndi zithuzi zomwe anaima ndi nkazi wake wake nthawi imeneyo ali oyembekezera, ulendo uno oyimbayu sanapangeso zakezi ndipo gulu latutumuka pomwe langouzidwa kuti kwabadwa mwana. Dan Lu pamodzi ndi nthiti yake Katerina Nzima lero alandira mphatso ya mwana wa mamuna zomwe anthu ochuluka adabwa […]
The post Banja la Dan Lu ladzidzimutsa gulu ndi mphatso ya mwana appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 