Mbava zitatu zomwe zimaba pobisalira gulewamkulu azilamula kukaseweza jere

Njonda zitatu zomwe zidanjatidwa pa mlandu okuba katundu zitavala ngati gulewamkulu kwa Chaima m’boma la Kasungu azipeza zolakwa pa mlandu wakuba ndipo  azilamula kukagwira ntchito ya kalavula gaga kwa zaka 12. Nkhani yonse ikuti njondazi  zitatuzi zomwe ndi a Sadarack Phiri azaka 48 zakubadwa, a Lazaro Nkhoma azaka 47  ndi a John Mkula azaka 35 […]

The post Mbava zitatu zomwe zimaba pobisalira gulewamkulu azilamula kukaseweza jere appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください