Bwalo la milandu ku Zomba lalephera kuyamba kumva mulandu wa mkulu wa bungwe la Malawi First a Bon Kalindo ndipo bwaloli lati mlanduwu uzayamba kumvedwa mwezi wa January chaka cha mawa 2024. A Kalindo amayenera kukawonekera ku bwalo la mulandu lero Lachitatu ku Zomba koma bwalo lalephera kuyamba kumva mulandu wao chifukwa Principal Resident Magistrate […]
The post Khoti ku Zomba lalephera kuyamba kumva mulandu wa Bon Kalindo appeared first on Malawi 24.