M’modzi wa akuluakulu a chipani cha DPP a Ken Msonda lero amafuna kukalanda katundu ku ofesi ya DHL ponena kuti kampaniyo inakanika kutumiza lita limodzi la mankhwala azitsamba obwezeretsera chitetezo mthupi omwe a Msonda amatumiza ku Botswana. Malingana ndi zomwe yalemba Zodiak, a Msonda pa 28 November chaka chino adapita ku ofesi ya DHL kukatumiza […]
The post A Msonda amafuna kulanda katundu ku DHL appeared first on Malawi 24.