Ngakhale kutenga nawo gawo pa ziwonetsero zili zonse uli ufulu wachibadwidwe, gulu lina lomwe likudzitchula kuti ‘Abwenzi a Atupele Muluzi’, lalangiza anthu m’dziko muno kuti asiye kutenga nawo gawo ponena kuti sizikubweretsa phindu ku dziko lino kamba koti otsogolerawo akumapanga pongofuna kukhutitsa mimba zawo. Akuluakulu agululi amayankhula izi lachinayi munzinda wa Blantyre pomwe anachititsa nsonkhano […]
The post Siyani kuchita nawo ziwonetsero, zilibe phindu – a Malawi alangizidwa appeared first on Malawi 24.