Apolisi m’dziko lino anjata a Shirieesh Betgiri yemwe ndi mkulu wapampando wakale wa kampani ya Salima Sugar kamba kokhudzidwa pa mlandu wakatangale wa ndalama zoposa K50 billion A Peter Kalaya omwe ndi mneneri wa apolisi m’dziko muno atsimikiza zankhaniyi ndipo iwo ati izi zadza pamene boma idachita kafukufuku ndipo malipoti adaonetsa kuti anthu ena adabera […]
The post Anjatidwa kamba kosayendetsa bwino ndalama appeared first on Malawi 24.