Anthu atatu amwalira pamene anthu ena asanu ndi m’modzi avulala pa ngozi yomwe yachitika dzulo madzulo m’boma la Nkhotakota Yemwe ndi mneneri wa apolisi m’bomali a Sub-Inspector Andrew Kamanga ati galimoto ya mtundu wa Sienta yomwe inanyamula anthuwa inagudubuzika itanyamula anthuwa munsewu wa M5. A Aaron Cement omwe amayendetsa galimotoli komanso wolandira ndalama m’galimotoli ndi […]
The post Anthu atatu afa galimoto itagudubuzika appeared first on Malawi 24.