Apolisi ku Zomba amanga njonda ziwiri chifukwa chothyola m’nyumba yosungiramo katundu ya mkulu wina ochita bizinezi pamsika wa 3 Miles ndi kubamo katundu wandalama zokwana K2.3 miliyoni. Njonda ziwirizi ndi a Thokozan Jackson a zaka 33 zakubadwa ndi a Own Luka azaka 28 zakubadwa. Mneneri wa apolisi m’bomali a Patricia Sipiliano atsimikiza za nkhaniyi ndipo […]
The post Awanjata kamba kothyola m’nyumba ndikubamo katundu wa K2.3 miliyoni appeared first on Malawi 24.