M’modzi mwa akatakwe omwe amatsatira bwino pa nkhani za ndale mdziko lino a Lydford Chadza ayamikira zomwe achita a Ken Msonda popepesa kwa mtsogoleri wa chipani cha DPP a Peter Mutharika ndipo iwo ati izi zaonetsa kukhwima mzeru pandale. A Chadza anafotokoza kuti mpungwepungwe ndi kusamvana komwe kunabuka sikukanatengera kwina kulikonse chipanichi. Kotero iwo apempha […]
The post Zomwe achita a Msonda zaonetsa kukhwima nzeru pandale, watero katakwe pandale appeared first on Malawi 24.