Apolisi m’boma la Ntchisi akusunga mchitokosi mnyamata wa zaka 16 atagwililira gogo wa zaka 74. Malingana ndi Mneneli wa apolisi ku chigawo cha pakati kum’mawa a Esther Mkwanda, nthawi ya kumasana pa tsikuli mnyamata anatsatila kumunda komwe gogoyu amakasaka nkhuni ndipo anamumanga manja ndi kukolopola zovala za gogoyu mkumuchita za kusalungamazo. Apolisi ati gogoyu anakafotokozera […]
The post Mnyamata wa zaka 16 wagwililira gogo wa Zaka 74 appeared first on Malawi 24.