A Ken Msonda omwe ndi membala wa komitiyi yaikulu ya chipani cha DPP apepesa kwa mtsogoleri wa chipanichi a Peter Mutharika pa zomwe iwo akhala akuchita ndipo pano ati akufuna a Mutharika atengenso mpando wa mtsogoleri wa chipani cha DPP. Izi zadza pomwe lero a Mutharika anayankhula mozaza ndikuwadzudzula a Msonda kuti akhoza kubwerela ku […]
The post A Ken Msonda apepesa kwa a Mutharika appeared first on Malawi 24.