Mwina anakadziwa a Ken Msonda sanakapita ku nkumano wa akuluakulu a chipani cha DPP (NGC) omwe ukuchitikira ku Mangochi chifukwa mtsogoleri wachipanichi a Peter Mutharika, wawasambitsa chokweza, kuwatsukuluza mpaka kuwauza kuti ngati samakonda chipanichi abwelere ku PP. Mu nkhani yathu m’mawa wa lero tinafotokoza kuti a Msonda omwe m’mbuyomu amaonetsa kuti ali mbali yomwe ikutsutsana […]
The post Zotsatira za NGC zayamba kufika: Mutharika wauza Msonda kuti atha kubwelera ku PP appeared first on Malawi 24.