Apolisi m’boma la Zomba amanga njonda ina kamba kopezeka ndi ma simukadi a lamya okwana 99 omwe njondayi imafuna kuti ilowetse mundende ya Zomba. Malingana ndi mneneri wa apolisi m’bomali, mkuluyi yemwe dzina lake ndi Tamani Sulumba wazaka 35 zakubadwa, anapita kundendeyi kuti akaone mzake yemwe adanjatidwa pamlandu wakuba. A Sulumba ananyamula botolo la mafuta […]
The post Wanjatidwa kamba kofuna kulowesa ma simukadi mu ndende appeared first on Malawi 24.