Kulinji ku DPP lero? Nsonkhano wa NGC

Dzulo lachiwiri tinasiyira poti khothi ku Lilongwe lakana kupeleka chiletso kwa Grezelder Jeffrey chomwe mwa zina chimafuna kuletsa mbali ya mtsogoleri wa chipanichi a Peter Mutharika kuchititsa msonkhano wa akuluakulu a chipani (NGC), ndipo titha kutsimikiza kuti msonkhanowu ulipo ku Mangochi lero, tiyeni tiyembekeze zambiri.  Akuluakulu a chipani cholamula chakalechi lero akhamukira ku hotela ya […]

The post Kulinji ku DPP lero? Nsonkhano wa NGC appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください