…wati kusolobana kwa zinthu vuto si atsogoleri M’busa wa mpingo wa God’s Chapel a Hastings Salanje omwe akuti posachedwapa anabedwa ndi zigandanga zomwe zimafuna K2 biliyoni kuti amasulidwe, wati dziko la Malawi likudutsa m’mavuto adzaoneni kamba koti nzika zake zambiri ndizoyipa, sizimalemekeza azitumiki ndipo wati anachoka m’dziko muno kamba komunamizira kuti amasungira ziwalo za anthu […]
The post A Malawi ambiri ndioyipa, mavutowo nchifukwa choti mumanyoza azitumiki a Mulungu – wakalipa Salanje appeared first on Malawi 24.