Kwatelera: khothi layimitsa konveshoni ya DPP

Dzuwa silingalowe osakambapo za chipani cha kale cholamura cha DPP ndipo pomwe tikudikira kuti mawa chipanichi chibweretsanji, kwa lero tasiyira poti khothi lalamura kuti zonse zomwe zinakambidwa kunkumano wa NGC omwe anaitanitsa a Grezelder Jeffrey zisachitike kaye, kuphatikiza konveshoni. Sabata yatha, a Jeffrey mwa mphamvu zawo ngati mlembi wamkulu wa chipani cha Democratic Progressive anaitanitsa […]

The post Kwatelera: khothi layimitsa konveshoni ya DPP appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください