Akuluakulu a mpingo wa God’s Chapel alengeza kuti zigawenga zomwe zinasowetsa mtsogoleri wawo Hastings Salanje masiku angapo apitawa, zamulavura tsopano ndipo ali bwino bwino. Pa 1 December chaka chino, akuluakulu a mpingo wa God’s Chapel anabwera poyera ndikulengeza kuti a Salanje abedwa ndi zigawenga zina pomwe iwo pamodzi ndi akuluakulu ena anali ndi zokambirana pa […]
The post ‘Zigawenga’ zamulavula Salanje appeared first on Malawi 24.