A polisi mu mzinda wa Lilongwe ku Area 3, anjata a Jonathan Nkhosa yemwe ndi mphunzitsi wa kupulayimale wa zaka 51 zakubadwa, kamba kobera anthu powanamiza kuti ndi wapolisi. A Nkhosa akhala akuchita bodza kwa abale a anthu omwe ali mkusungidwa mchitokosi cha apolisi powauza kuti alipire ndalama kuti m’bale wawo atuluke pa belo. Yemwe […]
The post Mphunzitsi wanjatidwa kamba kobela anthu ponena kuti ndi wapolisi appeared first on Malawi 24.