Ophunzira ku UNIMA akusowa ndalama ya chakudya komanso yolipilira nyumba

Ambiri mwa ophunzira omwe ali pangongole yaboma pasukulu ya ukachenjede ya UNIMA ati alipachiopsezo chosiyira maphunziro awo panjira kaamba kosowa ndalama yogulira zakudya komanso kulipilira nyumba zomwe iwo amakhala ngakhale kuti anasayinira ndalamayi ndibungwe lopereka ngongole la Higher Education Students’ Loans Board. M’modzi mwa ophunzirawa yemwe ali mchaka chachinayi chamaphunziro ake pa sukuluyi koma sanafune […]

The post Ophunzira ku UNIMA akusowa ndalama ya chakudya komanso yolipilira nyumba appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください