A Malawi awalangiza kuti asaononge ndalama mu nyengo ya khirisimasi

Akatswiri pa chuma achenjeza anthu m’dziko muno kuti apewe kuononga ndalama mwachisawawa mu nyengo ya khirisimasi komanso mu chikondwerero cha chaka cha tsopano kamba kamavuto a chuma amene ali dziko muno. M’modzi mwa akatswiriwa, a Lizzie Luhanga, ati anthu m’dziko muno ngati sasamalira ndalama zawo mu nyengo ya khirisimasi komanso mu chikondwerero cha chaka cha […]

The post A Malawi awalangiza kuti asaononge ndalama mu nyengo ya khirisimasi appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください