Mfumu Chidzalo ya ku Dowa yadzipha

Mfumu Chidzalo ya m’boma la Dowa, yomwe dzina lake lenileni ndi Moffat Lamulani Mlenga wa zaka 71, yadzimangirira itakanika kubweza ndalama za anthu amene inawalonjeza kuti idzawathandiza kugula fetereza otsika mtengo. Malingana ndi mneneri wa apolisi m’bomali, Sergeant Alice Sitima lachisanu nthawi ya 6 koloko m’mawa banja la mkuluyu linapita kumunda pomwe mfumuyi anali akugwira  […]

The post Mfumu Chidzalo ya ku Dowa yadzipha appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください