Boma lapereka chimanga ndi ndalama kwa omwe adakhudzidwa ndi Namondwe wa Freddy

Kutsatira mavuto omwe alipo kamba ka namondwe wa Freddy yemwe adaononga mbewu ndikuyika a Malawi ochuluka munjala yadzaoneni, tsopano boma layamba kugawa chimanga komanso ndalama m’madera omwe adakhudzidwa. Ntchito yopereka thandizoli yayambira mu mzinda wa Zomba komwe ntchitoyi yakhazikitsidwa. A Konja Mikana, m’modzi mwa omwe alandira nawo thandizoli, ati tsopano vuto lanjala lichepa. Archangel Bakolo […]

The post Boma lapereka chimanga ndi ndalama kwa omwe adakhudzidwa ndi Namondwe wa Freddy appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください