A Christopher Phiri azaka 40 zakubadwa yemwe ndi pulofeti wa mpingo wa Supernatural Embassy Ministrie, akusungidwa mchitokosi cha apolisi ku Mangochi kamba kogwililira mwana wawo obereka okha wazaka 16. Malipoti akusonyeza kuti m’busayu wakhala akuchita pakati pa miyezi ya Sepitembala ndi Novembala chaka chomwe chino. Malingana ndi kafukufuku wa apolisi, m’busayu banja lidatha ndi mkazi […]
The post Pulofeti amumanga kamba kogwililira mwana wake appeared first on Malawi 24.