Khoti lidzapereka chigamulo mwezi wamawa kwa Sing’anga oganizilidwa kuti anagwililira atsikana awiri

Bwalo la High Court ku Zomba likuyembekezeka kudzapereka chigamulo chake pa 19 January 2024 kwa Sing’anga wina Malizani Chibingu Paoneka yemwe akumuganizila kuti adagwililira atsikana awiri apachibale osakwana zaka 18 zakubadwa. Mu bwalo la milandu, oyimira Boma pamilandu adapempha bwalo kuti lipereke chilango chokhwima kwa Malizani Chibingu Paoneka chifukwa zomwe adachita ndidzosemphana ndi gawo 138 […]

The post Khoti lidzapereka chigamulo mwezi wamawa kwa Sing’anga oganizilidwa kuti anagwililira atsikana awiri appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください