Bwalo la milandu ku Zomba lalamula mamuna wina Andrea Nkula Masamba kuti akagwire ukaidi wakalavula gaga ku ndende kwa miyezi zaka 8 chifukwa chomupeza olakwa pamulandu ochita zamathanyula. Wapolisi oyimira Boma pamilandu Sub-Inspector Evelyn Dzoole adapempha bwalo kuti lipereke chilango chokhwima kwa Masamba chifukwa zomwe adachita pogonana ndi mamuna nzake ndizosemphana ndi malamulo a dziko […]
The post Bwalo lamilandu lalamula mamuna ochita zamathanyula kukakhala kundende zaka 8 appeared first on Malawi 24.