Asungwana okankha chikopa mu timu ya dziko lino ya Scorchers, akuyimba nyimbo ya Joseph Nkasa ya ‘Anamva’ pomwe akuti bungwe loyendetsa mpira la FAM silinawapatsebe ndalama zomwe linalonjeza kuphatikiza K10 miliyoni yomwe mneneri Shepherd Bushiri anafupa atsikanawa kuti agawane. Izi ndi malingana ndi zomwe tsamba lino lapeza pa masamba anchezo kuphatikizapo pa tsamba lotchuka lolemba […]
The post Lonjezo linadulitsa mutu wa Yohane: Osewera a Scorchers sanapatsidwebe ndalama zolonjezedwa appeared first on Malawi 24.