Tay Grin osadzaonekera ndi zingongo zako m’mutu, watero Mutale

Omwe ukumveka ndi kuoneka kuti ndi ubwezi pakati pa oyimba odziwika bwino mdziko muno Tay-Grin ndi mayi odziwika bwino wa mdziko la Zambia wafika pa m’nong’a pamene mayiyu wauza Nyau king kuti asapite kokaonekera ndi zingongo m’mutu. Polemba pa tsamba lake, Mutale Mwanza wati iye akulonjeza kudzakhala mayi wabwino wa ana a awiriwa ndipo amasangalatsidwa […]

The post Tay Grin osadzaonekera ndi zingongo zako m’mutu, watero Mutale appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください