Potsatira ziwawa zomwe ophunzira apa sukulu yaboma yogonera konko ya Ntcheu sekondale anachita lolemba, unduna owona za maphunziro m’dziko muno, watumiza ophunzira onse pasukuluyi ku tchuthi chokakamiza. Lolemba masana, pa 27 November, 2023 ophunzira ena pasukuluyi anayamba kugenda magalasi a malo ochitira zinthu zosiyanasiyana (hall) komaso ma ofesi a mphunzitsi wa mkulu pokwiya ndi zomwe […]
The post Ntcheu Sekondale ayitseka kaye appeared first on Malawi 24.