Chipani cha Democratic Progressive (DPP) chati kuchoka kwa mamembala a zipani zina omwe akuti alowa mu chipani cha DPP ndi chitsimikizo chakuti nzika zambiri za dziko lino zili ndi chikhulupiriro ndi chipani cha DPP. Gavanala wa chipanichi ku chigawo cha kum’mawa, Sheikh Emran Mtenje amayankhula izi dzulo ku Balaka pamene amalandira anthu okwana 76 omwe […]
The post A Malawi ali nafe chikhulupiriro — DPP appeared first on Malawi 24.