Anthu aulesi ndi omwe akutukwana Chakwera – watelo ‘prophet’ Habakkuk

…wafusa kuti kudzala sidi kwa mneneri ndikukapeleka kwa “mahule” chabwino nchiyani? Mneneri otchuka m’dziko muno, Habakkuk yemwe sanakhalepo pa banja koma akuti wachita zigololo kwambiri ndipo pano akudikira nthawi ya Mulungu kuti akwatile, wati sakuona chomwe mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera akulakwitsa kuti anthu adzimutukwana ndipo wafusa kuti kodi a Malawi mumafuna Chakwera-yo akubelekeni […]

The post Anthu aulesi ndi omwe akutukwana Chakwera – watelo ‘prophet’ Habakkuk appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください