Banki yaikulu mdziko muno ya Reserve yalangiza boma la Malawi komanso ma kampani omwe siaboma kuti asakweze malipiro a ogwira ntchito awo nsanga ponena kuti zitha kusokoneza chuma cha dziko lino. Izi zayankhulidwa lero mu mzinda wa Lilongwe komwe akuluakulu a banki yaikulu m’dziko muno ya Reserve anachititsa msonkhano wa atolankhani komwe anafotokoza zambiri zokhudza […]
The post Musawakwezere malipiro – yakuwa mokweza banki yaikulu appeared first on Malawi 24.