Sitikutulutsa 10,000 Kwacha, yatero RBM

Mkulu wa banki yaiyikulu m’dziko muno ya Reserve, a Wilson Banda, akana zoti bankiyi ikufuna kutulutsa K10,000 yogwirana. Polakhula ndi atolankhani a Wilson Banda anena kuti Bankiyi ilibeso maganizo otulutsa ndalamayi pakali pano ndipo zomwe zikuyenda masamba a mchezo ndi zabodza ndipo anthu asakhulupirire zimenezo. Iwo atsindika kuti bankiyi singatulutse ndalamayi chifukwa pakali pano ali […]

The post Sitikutulutsa 10,000 Kwacha, yatero RBM appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください