Chipwirikiti chidabuka dzulo madzulo kwa Chikanda, Kazembe, Mpondabwino mu mzinda wa Zomba apolisi ataphulitsa utsi okhetsa misozi pambuyo padziwonesero zomwe adatsogolera ndi mkulu wa gulu la Malawi First a Bon Kalindo. Zipolowezi zidayamba pomwe anthu ozungulira mdera la Mpondabwino adakathyola nyumba yawa polisi wina ndikubamo katundu komanso kuba mizimbe nkatikati mwa police college. Zipolowezi zidapitilira […]
The post Zipolowe zidabuka ku Zomba apolisi ataphulitsa utsi okhetsa misozi appeared first on Malawi 24.