Mtsogoleri wa mpingo wa Holy Palace Cathedral International, mneneri Rodrick Mtupa, wati kumayambiliro a chaka chino iye ananenera za ziwawa zomwe zachitika ku Limbe mu mzinda wa Blantyre ndipo wapempha anthu kuti apemphererebe dziko lino kwambiri. Malingana ndi mneneri Mtupa, kumayambiliro kwa chakachi Mulungu anamuuza kuti achenjeze dziko lino kudzera mu uneneri oti m’dziko muno […]
The post Zipolowe za ku Limbe ndinanenera kalekale – watelo mneneri Mtupa appeared first on Malawi 24.