Ndichitonzo kukweza malipiro ndi K10 pa K100 iliyonse, watero Kalindo

A Bon Kalindo omwe amachititsa zionetsero lero mu mzinda wa Blantyre apempha boma kuti likweze malipiro a anthu ogwira ntchito m’boma ndi K50 pa K100 iliyonse. A Kalindo, ati ndichitonzo  kukweza malipiro a ogwira ntchito m’boma ndi 10 Kwacha pa 100 Kwacha iliyonse kutengera kuti ndalama yadziko lino inagwa ndi 44 pelesenti. Iwo amayankhula izi […]

The post Ndichitonzo kukweza malipiro ndi K10 pa K100 iliyonse, watero Kalindo appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください