Patricia Kaliati yemwe ndi mlembi wamkulu wa chipani cha UTM wauza a Malawi kuti akuyenera kuyika maso komanso chiyembekezo pa a Saulos Chilima yemwe ndi mtsogoleri wachipanichi. A Kaliati amayankhula izi dzulo m’boma la Kasungu pamwambo olandira mamembala okwana 79 omwe ali adindo komanso anthu ena osiyanasiyana ochokera mzipani monga za AFORD, MCP ndi DPP. […]
The post Chiyembekezo cha a Malawi chikhale mwa a Chilima – atero a Kaliati appeared first on Malawi 24.