Kunali phazi thandize ku Limbe mu mzinda wa Blantyre pomwe ochita malonda m’mphepete mwa misewu anavumbulutsa miyala ndipo nawo ogendawo anafukizidwa komaso kuwubwira utsi okhetsa misozi. Izi zachitika lachiwiri pa 21 November, 2023 pomwe monga mwa nthawi zonse akuluakulu ochokera ku khonsolo ya Blantyre anapita mu msika wa Limbe kuti akathane ndi anthu onse omwe […]
The post A ‘City’ ayenda wa uyo-uyo ku Limbe appeared first on Malawi 24.