Sitinasinthe dzina, sitinagawanike – yatsutsa Great Angels Choir

…yafotokoza cholinga choitanira Kell Kay, Lulu ku ‘show’ ya ‘gospel’ Gulu loyimba nyimbo za uzimu m’dziko muno la Great Angels Choir latsutsa mwantu wa galu mphekesera zoti gululi lagawanika komaso kuti lasintha dzina lake kukhala New Manna International Ministries. Kuyambira sabata latha, m’masamba a nchezo mwakhala mukuyenda nkhani yoti gululi lasintha dzina ndipo onenawo amati […]

The post Sitinasinthe dzina, sitinagawanike – yatsutsa Great Angels Choir appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください