Ayambe kumbuyoko/Ayambe kumbuyoko kudzapeleka aaa/tiyeni tonse tikapeleke: Iyi ndi nyimbo yomwe akuimba anthu omwe alowa gulupu la pa ‘WhatsApp’ lomwe a kuti likusonkherana ndalama yoti Mai Mbambande akabweze kwa Triephornia Mpinganjira. Zoonadi, mbuto ya kalulu inakura nditadzaonani. Nkhaniyi yayambika kumathero asabata komweku pomwe nkazi wa khumutcha Thomson Mpinganjira, a Triephornia Mpinganjira anadzudzula bungwe la Mai […]
The post A Malawi kudzaipatsa moto! Akusonkha ndalama yoti Mai Mbambande akamubwezere Triephornia Mpinganjira appeared first on Malawi 24.