Ana akufuna chipepeso powachita mdulidwe makolo asakudziwa

Ana okwana 312 m’boma la Phalombe akamang’ala ku khothi kuti bungwe la Family Health Services (FHS) lomwe m’mbuyomu limatchedwa Population Services International (PSI) liwapepese ndi ndalama kamba kowachita mdulidwe makolo awo asakudziwa. Izi ndimalingana ndi nyuzipepala ya Weekend Nation yomwe yati anawa omwe ndiochokera mdera la mfumu yaiku Mkando, m’boma la Phalombe, anachitidwa mdulidwewu mu […]

The post Ana akufuna chipepeso powachita mdulidwe makolo asakudziwa appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください