Phungu wa chipani cha Malawi Congress Party m’dera lakumwera kwa boma la Dedza a Ishmael Onani, wabwereza kupeleka pempho lomwe a kuti anamutuma ndi anthu akudera lake loti mtundu wa mipando m’nyumba ya malamulo usinthidwe usakhaleso ‘blue’. A Onani amayankhula izi lachisanu pa 17 November pomwe aphungu anyumba ya malamulo akupitilira kuwunikira ndondomeko ya zachuma […]
The post Mipando ya ‘blue’ kuno ayi – phungu wati mtundu wa mipando ku nyumba ya malamulo usinthidwe appeared first on Malawi 24.