Mtsogoleri wakale wa dziko lino a Peter Mutharika ati ndondomeko zomwe ayika a Lazarus Chakwera pofuna kuthana ndi mavuto omwe akuta dziko la Malawi ndizochepa kwambili. Iwo ati mwandondomeko zina zomwe a Chakwera amayenera kuchita ndi monga kupereka ndalama ku masukulu awukanjende ndi cholinga choti pasakhale ophunzira osiya sukulu kamba ka fizi. A Mutharika anatinso […]
The post A Mutharika ati ndondomeko zomwe ayika a Chakwera ndizochepa appeared first on Malawi 24.