Chakwera akubwera lero

Mukaona mbendera petupetu, magetsi waliwali komaso apolisi atayima m’misewu, dziwani tate wa dziko lino wafika kuchokera kunja; a Lazarus Chakwera akubwera lero komatu apeza zinthu zambiri zakwera mtengo. Kapena a Chakwera abwera ndi mayankho? A Chakwera ananyamuka m’dziko muno Lachitatu kupita m’dziko la Saudi Arabia komwe amkayenera kukakhala nawo pa mkumano wa pakati pa mayiko […]

The post Chakwera akubwera lero appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください