Nzika ina ya m’boma la Ntcheu yadzudzula mkulu wa chitetezo wa mtsogoleri wakale wa dziko lino Peter Mutharika, a Norman Chisale, powuza dziko kuti anthu m’bomali diokwiya pakuzuzidwa kwa nzika zake zina. Izi zikudza pomwe posachedwapa a Norman Chisale omwe amachokera m’boma la Ntcheu, anauza wayilesi ya Zodiak kuti anthu m’bbomali ndiokwiya kwambiri kamba ka […]
The post Musatiipitsile mbiri, ife anthu aku Ntcheu sitinakutumeni – munthu wina wauza Norman Chisale appeared first on Malawi 24.